Zakudya za ziweto kuchokera chimanga
Uploaded 4 years ago | Loading

15:48
Reference book
Popanda mphweya, mapesi a chimanga chachiwisi odulidwa bwino amasakanikirana popanda kuwola. Izi zili choncho popeza tizilimbo ting’onoting’ono timadya zotsekemera zopezeka muchakudyachi, zomwe zimachititsa kuti chikhale nthawi yayitali.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya, UNIDO Egypt