Kudzala zinanazi pamodzi ndi nthochi ndi nyemba
Uploaded 4 years ago | Loading
13:29
Alimi aluso mdera lapakati ku Uganda amakhala ndi minda ya chonde ndipo amapewa kuswa mphanje nthawi zonse.Tiphunzira, ndipo tiwona momwe tingalimire zinanazi pamunda umodzi kwa zaka zisanu ndi chimodzi.Zinanazi zimayamba kubereka chaka chachiwiri mukadzala. Koma mukhoza kupeza ndalama podzala mbeu zina pakati pa mizere ya zinanazi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NOGAMU