<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kufunafuna mbozi zooneka ngati ntchembere zandonda

Uploaded 5 years ago | Loading

Kupopera mankhwala ndikolira ndalama zambiri ndipo sikungathetse vuto la mbozizi. Yenderani munda wanu kawiri pa sabata mu sabata zisanu ndi imodzi zoyambilira ndi kupha mazira ndi mbozi zonse zazing'ono ndi manja. Ndikwabwino kumayendera munda wanu chifukwa ngati simutero, ndithu simuzakhala ndi zokolola pakutha patsiku.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight and FAO
Share this video:

With thanks to our financial partners