Kupanga mafuta a mtedza komanso tokhwasula
Uploaded 4 years ago | Loading

12:04
Amayi a dziko la Benin akutiwonetsa zinthu zitatu zofunukira: kusankha mtundu wabwino wa mtedza, kutsatira ndondomeko zabwino pokolora komanso kusunga mtedza, komanso kutsatira ndondomeko zofunikira popanga mafuta ndi tokhwasula.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Alcide Agbangla