Kuthana ndi chuku Mu chimanga pamene chili m’munda komanso pokolola
Uploaded 4 years ago | Loading

14:00
Pogwiritisa ntchito manyowa komanso kubzala mwachangu, mbewu yanu imakhala ndi mphamvu komanso siyigwidwa ndi chuku.Chimanga chikauma, ndipo makoko akaoneka oyelera, kololani pasanadutse masabata awiri.Siyanitsani chimanga chabwino ndi choonongeka.Musayike chimanga pa dothi, chifukwa chitha kugwidwa ndi chuku ndi kuwononga chimanga ngakhale mutachisunga bwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight