Mbeu yabwino ya Mphodza
Uploaded 4 years ago | Loading

14:18
Ngati mbeu zanu muzikutira mu mankhwala zimamera mwa mphamvu ndi kutetezeka kumatenda. Mu kanema uyu tiphunzira kwa alimi aku India kasankhidwe kabwino ka mbeu ndi momwe amasamalira mbeu ndi mankhwala achilengedwe asanadzale.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, WOTR