Kukhala ndi nkhosa za thanzi
Uploaded 4 years ago | Loading
12:48
Pamakhala posavuta nkhosa kugwidwa ndi matenda monga Petse des Petits Ruminants omwe amatchedwanso mlili wa nkhosa, komanso pasteurellosis ndi majeremusi. Nkhosa yodwala siikula msanga ndipo imagulitsidwa pa mtengo otsika chifukwa imakhala yoonda ndipo nyama yake yopanda nthazi. Kuyendera nkhosa pafupipafupi kumakuthandiza kudziwa msanga matenda a khosazo.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD