Kukolora, kuyanikandikusunga soya
Uploaded 7 years ago | Loading

7:29
Mbewuya soya yosakololedwa bwino ndiyo sasungidwa bwino imataya mphamvu yomerera chifukwa chinyotho ndi kutentha kumapha moyo wambewu. Mbewu zonyowa kapena zokhala ndinguwi zimaola pamene zikusungidwa. Mukanema iyi, tikambirana zakukolola soya, kuumitsa, kupeta, kusakha ndi kusunga.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
DEDRAS