Kupanga ufa wa nthochi
Uploaded 8 years ago | Loading
11:45
Anthu padziko lonse amadya nthochi. Pamene anthu ena amadzidya ngati chakudya chokhutitsa, ena amasankha kungozidya ngati chipatso chabe. Mukakolola, sizichedwa kuonongeka komansotu zimatha kuonongeka posamusa ndi yosunga. Komatu ndizotheka kupanga chakudya china chopatsa thanzi kuchokera ku nthochi. Chakudyachi ndi ufa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
KENAFF, Farm Radio Trust Malawi, UNIDO Egypt, Farmers Media Uganda