Kupanga zokometsera ndiwo kuchokera ku soya
Uploaded 4 years ago | Loading
9:57
Kumadzulo kwa Africa, kuli zokometsera ndiwo zosiyanasiya zopangidwa ku njere za mtengo wa Néré omwe umatchedwanso mtengo wa zombe. Ku Mali, tokometserati timatchedwa Soumbala. Kamba kodula mitengo mwachisawasawa ku chipululu cha sahel, mtengo wa soumbala umasowa komanso ngokwera mtengo. Ngakhale amapezeka koma amayi ena ku Mali apeza njira yina yopangira soumbala kuchokera ku mbeu ya soya.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD