Kapangidwe ka nazale ya Tsabola
Uploaded 8 years ago | Loading
13:33
Mu kanema uyu tiphunzitsana za momwe tingapangile nazale ndi mabedi a sabola kuti pamapeto pake mukhale ndi mbewu zanthanzi ndi zopilila ku matenda.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight