Nyelele zofiira kuthana ndi atongole
Uploaded 3 years ago | Loading
11:00
Reference book
Zimangotenga phindi zochepa kuti atongole apeze malo kuti abaye chipatso ndikuyikira dzira kukhokho la chipatso.Koma mu nthawi yochepa, nyelelezi zimathamangitsa atongole kapena kuwagwira, monga mmene tiphunzilire kuchokera kwa katswiri odzala ma manachesi.Kuti mumvetse izi, tiphunzire zambiri za nyelelezi.Nyelelezi zimalumikizana potulutsa fungo komanso pokhudzana munjira yapadera-dera.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight