<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kudyetsa nkhuku za hybrid

Uploaded 4 years ago | Loading

Tingakwaniritse zofuna za nkhuku podzipatsa zomera zobiliwira. Akhoza kukhala masamba ongothyoledwa kumene kapena zipatso.Ngati tikufuna nkhuku zathu zizikula bwino, ndibwino kudzipatsa zakudya zogula zokhala ndi kasakaniza wa madeya, cake ya mafuta ndi kasakaniza wa mbeu zagulu la chimanga.

Current language
Chichewa / Nyanja
Categories
Produced by
AMEDD, DEDRAS, MOBIOM, Songhaï Centre
Share this video:

With thanks to our financial partners