Kudzala soya pa mlingo oyenera
Uploaded 4 years ago | Loading
10:49
Mu kanema uyu tiona momwe mungadzalire soya pa mlingo oyenera kuti mupeze zokolola zochuluka ndi ndalama.Tikuyenera kuganizira zinthu zinayi izi:Gwiritsani ntchito mbeu yomera bwino;Chepetsani mpata pakati pa mizere ndi mapando;Musaponde mu mapando;Chepetsani mbewa zomwe zimadya mbeu mukangodzala.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
DEDRAS