Mphala la chiponde lotsakaniza ndi zokometsera
Uploaded 6 years ago | Loading
12:20
Zakudya monga nseula kapena soya zimathandiza kumanga thupi. Muzakudyazi mumakhalanso mafuta othandiza kuti mwana anenepe. Zipatso ndi masamba zimakhala ndi michere yopatsa thanzi ndi kulimbitsa thupi imene imafunika kuti mwana akule. Zipatso zowawasa zimakhala ndi vitamini C yemwe amathandiza thupi kusungunula mchere wa iron. Titha kupeza zakudyazi kumbewu zomwe timalima kapena zomwe timathyola kutchire.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD