Kuimikira ndi kudulira magalagadeya
Uploaded 1 year ago | Loading
8:03
Munda wa magalagadeya osamalidwa bwino umatha kupatsa alimi phindu chaka chonse. Mukanema uyu, tiphunzira kuimikira ndi kudulira kwabwino kwa magalagadeya kuti mukolore zochuluka.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NOGAMU, Sulma Foods Uganda