<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Kumanga Khola la M’mwamba la Nkhosa ndi mbuzi

Uploaded 3 years ago | Loading

M’makola ambiri, nkhosa kapena mbuzi zimakhala padothi. Ziwetozi zimagona mu mkodzo ndi ndowe zake. Chifukwa chosowa ukhondo, zambiri zimadwala.M’kanema uyu, tiwona momwe mungakonzere thandala loyika mu khola,  kuti khola lanu likhale lam’mwamba.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action, Bangladesh and Nepal, Christian Commission for Development in Bangladesh (CCDB)
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors