<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Nazale ya anyezi

Uploaded 4 years ago | Loading

Nazale ya anyezi imafuna nthaka yabwino komanso yofewa. Thirani manyowa ocha bwino. Mu nyengo yamvula, kwezani mabedi anu kuti nazale zanu zisaole. Mukagwilitsa ntchito mbewu yabwino, zambiri zimamela ndipo simufunika njere zambiri. Nazale za anyezi zimafunika mpata okwanira kuti zikule, choncho musayandikitse pofesa. Fesani njere mmizere yampata wa masentimita 5 mapaka 10 ndi sentimita imodzi kulowa pansi. Wazani pamwaba kadonthii kofewa bwino. Kanemayu akukambanso za kugwiritsa ntchito feteleza.

Current language
Chichewa / Nyanja
Categories
Produced by
Agro-Insight
Share this video:

With thanks to our financial partners