Kulimbikitsa kukhala ndi nyelele mmunda wanu wa zipatso
Uploaded 4 years ago | Loading
13:00
Reference book
Nyelele zofiira ndi bwenzi la alimi. Zimateteza zipatso ku atongole ndi tizilombo tina.Ngati mulibe nyelele zofiila zimenezi mmunda wanu, tolerani zitsa ndi kukadziyika mu umodzi mwa mitengo ya zipatso zanu.Thandizani nyelele kupita mitengo yina pomanga chingwe kapena kuyala kamtengo kulumikiza mitengo yoyandikana
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight