Kupanga juice kuchokera ku chipatso cha Nkholoso
Uploaded 4 years ago | Loading

9:20
Dziko lonse, anthu amakonda nthangala zake, kusiyana ndi chipatso. Komabe mukhoza kupanga juice kuchokera ku chipatso cha nkholoso komanso zakudya zina zimene zikhoza kudyedwa chaka chonse.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
DEDRAS