kupanga chakudya chamaguru cha ng’ombe za mkaka
Uploaded 3 years ago | Loading
8:37
Reference book
Kutengera ndi mkaka omwe ng’ombe ikutulutsa, mutha kuwerengera mlingo wa chakudya chamaguru chomwe imafuna.Mudzidyetsanso ng’ombe yanu udzu obiliwira tsiku ndi tsiku. Izi zimathandiza kuchulukitsa mkaka komanso mafuta mumkakamo. Zimathandizanso kugayabwino chakudya
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action, Nepal